Genesis 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Abulamu atapatukana ndi Loti, Yehova anamuuza kuti: “Takweza maso ako kuchokera pamene ulipo. Uyang’ane kumpoto ndi kum’mwera, komanso kum’mawa ndi kumadzulo.+
14 Abulamu atapatukana ndi Loti, Yehova anamuuza kuti: “Takweza maso ako kuchokera pamene ulipo. Uyang’ane kumpoto ndi kum’mwera, komanso kum’mawa ndi kumadzulo.+