Chivumbulutso 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000. Chivumbulutso 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdyerekezi,+ amene anali kuwasocheretsa, adzaponyedwa m’nyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wonyenga uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa usana ndi usiku kwamuyaya.
2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000.
10 Mdyerekezi,+ amene anali kuwasocheretsa, adzaponyedwa m’nyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wonyenga uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa usana ndi usiku kwamuyaya.