Machitidwe 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo onse analira kwambiri, ndipo anakumbatira+ Paulo ndi kumupsompsona mwachikondi.+