Genesis 30:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipatseni akazi anga ndi ana anga amene ndakugwirirani ntchito kuti ndizipita, pakuti inuyo mukudziwa ntchito imene ndakugwirirani.”+ Hoseya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yakobo anathawira kumunda wa ku Siriya+ ndipo Isiraeli+ anapitirizabe kugwira ntchito+ ndi kulondera nkhosa kuti apeze mkazi.+
26 Ndipatseni akazi anga ndi ana anga amene ndakugwirirani ntchito kuti ndizipita, pakuti inuyo mukudziwa ntchito imene ndakugwirirani.”+
12 Yakobo anathawira kumunda wa ku Siriya+ ndipo Isiraeli+ anapitirizabe kugwira ntchito+ ndi kulondera nkhosa kuti apeze mkazi.+