Aefeso 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwiyani, koma musachimwe.+ Dzuwa lisalowe muli chikwiyire,+ Akolose 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu amuna, musaleke kukonda akazi+ anu ndipo musamawapsere mtima kwambiri.+