1 Akorinto 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ngakhale utakwatira, sikuti uchimwa.+ Ndipo ngati amene sali pabanja* walowa m’banja, sikuti wachimwa. Komabe, olowa m’banjawo adzakhala ndi nsautso m’thupi mwawo.+ Choncho ine ndikukutetezani.
28 Koma ngakhale utakwatira, sikuti uchimwa.+ Ndipo ngati amene sali pabanja* walowa m’banja, sikuti wachimwa. Komabe, olowa m’banjawo adzakhala ndi nsautso m’thupi mwawo.+ Choncho ine ndikukutetezani.