Ekisodo 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Muzichita chikondwerero cha masabata ndi tirigu woyamba kucha pa nyengo yokolola tiriguyo.+ Muzichitanso chikondwerero cha zokolola kumapeto kwa chaka.+ Yohane 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kodi inu simunena kuti kwatsala miyezi inayi kuti tiyambe kukolola? Koma ndikuti: Kwezani maso anu muone m’mindamo, mwayera kale ndipo m’mofunika kukolola.+ Moti pano
22 “Muzichita chikondwerero cha masabata ndi tirigu woyamba kucha pa nyengo yokolola tiriguyo.+ Muzichitanso chikondwerero cha zokolola kumapeto kwa chaka.+
35 Kodi inu simunena kuti kwatsala miyezi inayi kuti tiyambe kukolola? Koma ndikuti: Kwezani maso anu muone m’mindamo, mwayera kale ndipo m’mofunika kukolola.+ Moti pano