Genesis 30:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yakobo anamuyankha Labani kuti: “Inuyo mukudziwa ntchito imene ndakugwirirani, ndiponso mmene ndasamalira ziweto zanu.+ Aefeso 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 pakuti mukudziwa kuti chabwino chilichonse chimene wina aliyense angachite adzachilandiranso kwa Yehova,+ kaya munthuyo akhale kapolo kapena mfulu.+ Akolose 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,
29 Yakobo anamuyankha Labani kuti: “Inuyo mukudziwa ntchito imene ndakugwirirani, ndiponso mmene ndasamalira ziweto zanu.+
8 pakuti mukudziwa kuti chabwino chilichonse chimene wina aliyense angachite adzachilandiranso kwa Yehova,+ kaya munthuyo akhale kapolo kapena mfulu.+
23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,