Yobu 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zamoyo zonse zimafera limodzi,Ndipo munthu amabwerera kufumbi.+ Mlaliki 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zonse zimapita kumalo amodzi.+ Zonse zinachokera kufumbi+ ndipo zonse zimabwerera kufumbi.+