Genesis 30:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Motero ziweto zazikazi zikaona timitengoto zinali kutenthadi thupi kukonzekera kutenga bere. Zikatero, zinali kuswa ana amizeremizere ndi amawangamawanga.+
39 Motero ziweto zazikazi zikaona timitengoto zinali kutenthadi thupi kukonzekera kutenga bere. Zikatero, zinali kuswa ana amizeremizere ndi amawangamawanga.+