Genesis 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yakobo anadzuka m’mawa kwambiri, n’kutenga mwala umene anautsamira uja, n’kuuimika monga mwala wachikumbutso. Atatero anauthira mafuta pamwamba.+ Genesis 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero, Yakobo anaimika mwala wachikumbutso pamalo pamene anali kulankhula nayepo,+ kenako pamwalawo anathirapo nsembe yachakumwa ndi mafuta.+
18 Tsopano Yakobo anadzuka m’mawa kwambiri, n’kutenga mwala umene anautsamira uja, n’kuuimika monga mwala wachikumbutso. Atatero anauthira mafuta pamwamba.+
14 Zitatero, Yakobo anaimika mwala wachikumbutso pamalo pamene anali kulankhula nayepo,+ kenako pamwalawo anathirapo nsembe yachakumwa ndi mafuta.+