Genesis 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+ Yobu 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ng’ombe zawo zamphongo zimapereka bere, ndipo siziwononga mphamvu zobereketsa.Ng’ombe zawo zazikazi zimabereka+ ndipo sizibereka ana akufa.
27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+
10 Ng’ombe zawo zamphongo zimapereka bere, ndipo siziwononga mphamvu zobereketsa.Ng’ombe zawo zazikazi zimabereka+ ndipo sizibereka ana akufa.