Genesis 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yakobo anadzuka m’mawa kwambiri, n’kutenga mwala umene anautsamira uja, n’kuuimika monga mwala wachikumbutso. Atatero anauthira mafuta pamwamba.+
18 Tsopano Yakobo anadzuka m’mawa kwambiri, n’kutenga mwala umene anautsamira uja, n’kuuimika monga mwala wachikumbutso. Atatero anauthira mafuta pamwamba.+