Genesis 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano Yakobo anakweza maso ake n’kuona Esau akubwera limodzi ndi amuna 400.+ Ataona choncho, anagawa ana ake n’kuwapereka kwa Leya, kwa Rakele, ndi kwa akapolo ake awiri aja.+
33 Tsopano Yakobo anakweza maso ake n’kuona Esau akubwera limodzi ndi amuna 400.+ Ataona choncho, anagawa ana ake n’kuwapereka kwa Leya, kwa Rakele, ndi kwa akapolo ake awiri aja.+