10 Koma Yakobo anati: “Ayi chonde, musatero. Ngati mwandikomeradi mtima,+ landirani mphatso yangayi, popeza cholinga chake chinali chakuti ndione nkhope yanu, ndipo ndaionadi. Zili ngati ndaona nkhope ya Mulungu, chifukwa mwandilandira ndi manja awiri.+