Ekisodo 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 pamenepo muzidzapereka kwa Yehova mwana aliyense woyamba kubadwa,+ ndi mwana aliyense wa ziweto zanu woyamba kubadwa.+ Chachimuna chilichonse n’cha Yehova.+
12 pamenepo muzidzapereka kwa Yehova mwana aliyense woyamba kubadwa,+ ndi mwana aliyense wa ziweto zanu woyamba kubadwa.+ Chachimuna chilichonse n’cha Yehova.+