Genesis 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna wobadwa kwa Ada mkazi wake wa Esau, komanso Reueli, mwana wamwamuna wobadwa kwa Basemati mkazi wake wa Esau.+
10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna wobadwa kwa Ada mkazi wake wa Esau, komanso Reueli, mwana wamwamuna wobadwa kwa Basemati mkazi wake wa Esau.+