Genesis 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nawa ana a Reueli, mwana wamwamuna wa Esau: Mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Shama ndi mfumu Miza. Amenewa ndiwo anali mafumu a kubanja la Reueli m’dziko la Edomu.+ Iwowa anali ana obadwa kwa Basemati mkazi wa Esau.
17 Nawa ana a Reueli, mwana wamwamuna wa Esau: Mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Shama ndi mfumu Miza. Amenewa ndiwo anali mafumu a kubanja la Reueli m’dziko la Edomu.+ Iwowa anali ana obadwa kwa Basemati mkazi wa Esau.