1 Mbiri 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Patapita nthawi, Shauli anamwalira ndipo Baala-hanani mwana wa Akibori+ anayamba kulamulira m’malo mwake.
49 Patapita nthawi, Shauli anamwalira ndipo Baala-hanani mwana wa Akibori+ anayamba kulamulira m’malo mwake.