Genesis 34:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma anawo anayankha kuti: “Kodi ndi bwino kuti munthu azitenga mlongo wathu ngati hule?”+ Numeri 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mkazi wa munthu angazembere mwamuna wake n’kumuchimwira+
12 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mkazi wa munthu angazembere mwamuna wake n’kumuchimwira+