Genesis 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inuyo a Farao munatikwiyira kwambiri ife atumiki anu.+ Ineyo ndi mkulu wa ophika mkate munatitsekera m’ndende ya kunyumba kwa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+
10 Inuyo a Farao munatikwiyira kwambiri ife atumiki anu.+ Ineyo ndi mkulu wa ophika mkate munatitsekera m’ndende ya kunyumba kwa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+