Genesis 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komabe, zonse zikadzakhala bwino kwa iwe usadzandiiwale.+ Chonde, udzandikomere mtima ponditchula kwa Farao,+ ndipo ukayesetse kuti ndidzatuluke m’ndende muno. Yobu 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anzanga apamtima anditaya.+Anthu amene ndinali kuwadziwa andiiwala,
14 Komabe, zonse zikadzakhala bwino kwa iwe usadzandiiwale.+ Chonde, udzandikomere mtima ponditchula kwa Farao,+ ndipo ukayesetse kuti ndidzatuluke m’ndende muno.