Genesis 41:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma zitadya zinzakezo, mimba za ng’ombe zowondazo sizinaoneke kuti mwalowa kanthu, popeza ng’ombezo zinaonekabe zowonda ngati poyamba.+ Pamenepo ndinagalamuka. 1 Mafumu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Solomo atagalamuka,+ anazindikira kuti waona masomphenya. Kenako anapita ku Yerusalemu n’kukaimirira pamaso pa likasa+ la pangano la Yehova. Ndiyeno anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano+ n’kukonzera phwando+ atumiki ake onse.+
21 Koma zitadya zinzakezo, mimba za ng’ombe zowondazo sizinaoneke kuti mwalowa kanthu, popeza ng’ombezo zinaonekabe zowonda ngati poyamba.+ Pamenepo ndinagalamuka.
15 Solomo atagalamuka,+ anazindikira kuti waona masomphenya. Kenako anapita ku Yerusalemu n’kukaimirira pamaso pa likasa+ la pangano la Yehova. Ndiyeno anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano+ n’kukonzera phwando+ atumiki ake onse.+