Yeremiya 52:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehoyakini anavula zovala zake za kundende,+ ndipo nthawi zonse anali kudya chakudya+ pamaso pa mfumuyo masiku onse a moyo wake.+
33 Yehoyakini anavula zovala zake za kundende,+ ndipo nthawi zonse anali kudya chakudya+ pamaso pa mfumuyo masiku onse a moyo wake.+