Genesis 43:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pobwerera, zinachitika n’zakuti, titafika pamalo ogona+ n’kumasula matumba athu, tinangoona kuti ndalama za aliyense zili pakamwa pa thumba lake, zonse malinga ndi kulemera kwake. Choncho tabwera nazo kuti tizibweze tokha.+
21 Pobwerera, zinachitika n’zakuti, titafika pamalo ogona+ n’kumasula matumba athu, tinangoona kuti ndalama za aliyense zili pakamwa pa thumba lake, zonse malinga ndi kulemera kwake. Choncho tabwera nazo kuti tizibweze tokha.+