Genesis 42:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati mulidi achilungamo, mmodzi wa inu atsale m’ndendemu.+ Ena nonsenu pitani, mukapereke tirigu kunyumba zanu chifukwa kuli njala.+
19 Ngati mulidi achilungamo, mmodzi wa inu atsale m’ndendemu.+ Ena nonsenu pitani, mukapereke tirigu kunyumba zanu chifukwa kuli njala.+