1 Mbiri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Isakara analipo anayi: Tola,+ Puwa,+ Yasubi, ndi Simironi.+