Numeri 26:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Yezera+ amene anali kholo la banja la Ayezera, ndi Silemu+ amene anali kholo la banja la Asilemu.