Nehemiya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ena anali kunena kuti: “Tikumapereka ana athu aamuna ndi ana athu aakazi monga chikole kuti tipeze chakudya ndi kukhala ndi moyo.”+ Maliko 8:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 N’chiyani kwenikweni chimene munthu angapereke chosinthanitsa ndi moyo wake?+
2 Ena anali kunena kuti: “Tikumapereka ana athu aamuna ndi ana athu aakazi monga chikole kuti tipeze chakudya ndi kukhala ndi moyo.”+