Ezara 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Amuna inu mudziwe kuti ansembe,+ Alevi,+ oimba,+ alonda a pakhomo,+ Anetini,+ ndi anthu ogwira ntchito panyumba ya Mulunguyi, musawakhometse msonkho umene munthu aliyense amakhoma, msonkho wakatundu,+ kapena msonkho wapanjira.+
24 Amuna inu mudziwe kuti ansembe,+ Alevi,+ oimba,+ alonda a pakhomo,+ Anetini,+ ndi anthu ogwira ntchito panyumba ya Mulunguyi, musawakhometse msonkho umene munthu aliyense amakhoma, msonkho wakatundu,+ kapena msonkho wapanjira.+