Genesis 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Salimo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi M’busa wanga.+Sindidzasowa kanthu.+ 1 Petulo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.
13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+
25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.