Deuteronomo 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Rubeni akhale ndi moyo, asafe ayi,+Ndipo anthu ake asakhale ochepa.”+