Genesis 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12.
22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12.