Genesis 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Rakele anati: “Nayu kapolo wanga Biliha.+ Mugone naye kuti andiberekere mwana woti akhale wanga,* kuti ineyonso ndikhale ndi ana kuchokera kwa iye.”+
3 Kenako Rakele anati: “Nayu kapolo wanga Biliha.+ Mugone naye kuti andiberekere mwana woti akhale wanga,* kuti ineyonso ndikhale ndi ana kuchokera kwa iye.”+