Miyambo 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngakhale dzanja ligwirane ndi dzanja linzake, munthu woipa sadzapewa chilango,+ koma ana a anthu olungama adzapulumuka ndithu.+ 2 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaperekanso chilango padziko lakale lija ndipo sanalilekerere,+ koma anasunga Nowa, mlaliki wa chilungamo,+ pomupulumutsa pamodzi ndi anthu ena 7,+ pamene anabweretsa chigumula+ padziko la anthu osaopa Mulungu.
21 Ngakhale dzanja ligwirane ndi dzanja linzake, munthu woipa sadzapewa chilango,+ koma ana a anthu olungama adzapulumuka ndithu.+
5 Anaperekanso chilango padziko lakale lija ndipo sanalilekerere,+ koma anasunga Nowa, mlaliki wa chilungamo,+ pomupulumutsa pamodzi ndi anthu ena 7,+ pamene anabweretsa chigumula+ padziko la anthu osaopa Mulungu.