Levitiko 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Cholengedwa chilichonse pakati pa nyama, chimene chili ndi ziboda zogawanika zokhala ndi mpata pakati, chomwenso chimabzikula, n’chimene mungadye.+ Deuteronomo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya nyama zimene muyenera kudya ndi izi:+ ng’ombe, nkhosa, mbuzi,
3 Cholengedwa chilichonse pakati pa nyama, chimene chili ndi ziboda zogawanika zokhala ndi mpata pakati, chomwenso chimabzikula, n’chimene mungadye.+