Genesis 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno chimvula chinakhuthuka padziko lapansi kwa masiku 40 usana ndi usiku.+