Genesis 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Madziwo anapitirizabe kuwonjezeka koopsa padziko lapansi, ndipo chingalawachonso chinapitirizabe kuyandama pamwamba pa madzi.+
18 Madziwo anapitirizabe kuwonjezeka koopsa padziko lapansi, ndipo chingalawachonso chinapitirizabe kuyandama pamwamba pa madzi.+