Genesis 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Madziwo anakwera kwambiri kupitirira mapiri ataliataliwo ndi mikono 15.+ Genesis 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso madzi anali kuchepa pang’onopang’ono padziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madziwo anali atachepa ndithu.+
3 Komanso madzi anali kuchepa pang’onopang’ono padziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madziwo anali atachepa ndithu.+