Genesis 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Mulungu anati: “Dziko lapansi+ likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta,+ nyama zokwawa,*+ komanso nyama zakutchire+ monga mwa mitundu yake.” Ndipo zinaterodi. Genesis 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo cholengedwa chilichonse chamoyo cha padziko lapansi, cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, chilichonse chokwawa padziko lapansi, ndi nsomba zonse za m’nyanja, zizikuopani. Tsopano ndapereka zonsezi m’manja mwanu.+
24 Tsopano Mulungu anati: “Dziko lapansi+ likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta,+ nyama zokwawa,*+ komanso nyama zakutchire+ monga mwa mitundu yake.” Ndipo zinaterodi.
2 Ndipo cholengedwa chilichonse chamoyo cha padziko lapansi, cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, chilichonse chokwawa padziko lapansi, ndi nsomba zonse za m’nyanja, zizikuopani. Tsopano ndapereka zonsezi m’manja mwanu.+