Genesis 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+ Yesaya 54:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+
17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+
9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+