Genesis 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+
29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+