Genesis 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atatuwa ndiwo anali ana a Nowa. Ndipo anthu onse amene ali padziko lapansi anachokera mwa iwowa.+