Salimo 120:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+ Ezekieli 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Kumeneko kulinso dziko la Meseke,+ Tubala+ ndi makamu awo onse. Manda awo ali mozungulira mfumu yawo. Onsewa ndi anthu osadulidwa, anthu olasidwa ndi lupanga chifukwa chakuti anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.
5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+
26 “‘Kumeneko kulinso dziko la Meseke,+ Tubala+ ndi makamu awo onse. Manda awo ali mozungulira mfumu yawo. Onsewa ndi anthu osadulidwa, anthu olasidwa ndi lupanga chifukwa chakuti anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.