Genesis 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ake, kuti: “Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi.+ Luka 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Wachita zamphamvu ndi dzanja lake,+ wabalalitsira kutali odzikweza m’zolinga za mitima yawo.+