Genesis 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aripakisadi anabereka Shela+ ndipo Shela anabereka Ebere. 1 Mbiri 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aripakisadi anabereka Shela,+ ndipo Shela anabereka Ebere.+ Luka 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 mwana wa Serugi,+mwana wa Reu,+mwana wa Pelegi,+mwana wa Ebere,+mwana wa Shela,+