Genesis 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nayenso Semu, kholo la ana onse a Ebere,+ anali ndi mbadwa zake. Semu anali mng’ono wake wa Yafeti, amene anali wamkulu pa onse. 1 Mbiri 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aripakisadi anabereka Shela,+ ndipo Shela anabereka Ebere.+
21 Nayenso Semu, kholo la ana onse a Ebere,+ anali ndi mbadwa zake. Semu anali mng’ono wake wa Yafeti, amene anali wamkulu pa onse.