Genesis 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anamuuzanso kuti: “Ine ndine Yehova, amene ndinakuchotsa ku Uri wa kwa Akasidi, kudzakupatsa dzikoli kuti likhale lako.”+ Nehemiya 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ ndi kum’tulutsa ku Uri wa Akasidi+ ndipo munamutcha dzina lakuti Abulahamu.+
7 Anamuuzanso kuti: “Ine ndine Yehova, amene ndinakuchotsa ku Uri wa kwa Akasidi, kudzakupatsa dzikoli kuti likhale lako.”+
7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ ndi kum’tulutsa ku Uri wa Akasidi+ ndipo munamutcha dzina lakuti Abulahamu.+