Genesis 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 N’chifukwa chiyani unanena kuti, ‘Ndi mlongo wanga,’+ moti ndinatsala pang’ono kumutenga kukhala mkazi wanga? Nayu tsopano mkazi wako. Mutenge uzipita!”
19 N’chifukwa chiyani unanena kuti, ‘Ndi mlongo wanga,’+ moti ndinatsala pang’ono kumutenga kukhala mkazi wanga? Nayu tsopano mkazi wako. Mutenge uzipita!”