Genesis 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano Yehova Mulungu anatenga munthu uja n’kumuika m’munda wa Edeni+ kuti aziulima ndi kuusamalira.+
15 Tsopano Yehova Mulungu anatenga munthu uja n’kumuika m’munda wa Edeni+ kuti aziulima ndi kuusamalira.+